Atsikana awiri ochita khalidwe loyendayenda ndilokonda kupakulisa kwa zidyamakanda mu nzinda wa Lilongwe, Riana Baggus ndi Patience Mwala, akutsadzulana ku WhatsApp kamba ka mchitidwe wachimasomaso. Oyamba akumveka ngati amakhala Kwa Mtsilizayo nde Riana.