
hiiii kaya
@its_stv • 4,162 subscribers
MULUNGU PALIBE CHOMULAKA
Videos

mmodzi mwa anyamata anayi omwe agwidwa atakhara akusakidwa kwa nthawi yayitali ndi anthu omwe amawabera Ndalama zomwe adyera anthu zikuposa K700 million. Ndipo agwadwira ku Neno, iwowa amati akafika pamalo amapanga zomwe akufuna akamaliza amalipira koma payment imakhara ya fake.
hiiii kaya87,027 Aufrufe • vor 3 Monaten
Keine weiteren Inhalte verfügbar