10 Comments
Comments from the original post on X (Twitter)

@mapulukutu
So Malawi Government Officials visit North Korea???? Really???🤔🤔
5 likes

@JShulu
Ena akuti anadabwa ndi thupi la m'bale wawo m'mene linaonekela
3 likes

@JShulu
Ongopanga exhume ma bodies anthuwa tisimikize. Akuti ambiri sanaonetse nkhope zawo.
3 likes

@CchikalipoP
The body needs to be exhumed by all means… There is something here and he was saying something to his wife, indirectly….
3 likes

@Time4us8
That in our lifetime, we will see the tail end of this injustice, is yet to be seen. #Chikangawa #Courage #Malawi #SaulosChilima
2 likes

@RKhataza
So touching narrative with many questions.
1 like

@SizibaSizw95476
Mayiwa ndi amene ayamba kupeleka chithunzi choona pa zomwe zinachitika ku thungwa, kenako Duma ndi amene anadzatulutsa chithunzi chinanso. Flora Mkandawire ndi winanso, osati zifwamba zaku MDF zija mogwirizana ndi MCP .
1 like

@Gkace_GK
This is very painful and heavy. Let the truth come out.

@JNsona79755
He definitely sacrificed himself for the family

@ImediWillex
Iyiyi pofunika Hon Nyamilandu and his commitee members ayiyang'ane mwachidwi
