Loading video...
Video Failed to Load
Zinazi mumaziputa dala
29,650 views • 12 days ago •via X (Twitter)
17 Comments

Honest question, ndikufuna kudziwa nawo. Kodi military uniform imakanizidwa kuti civilian asavale chifukwa chan? Ndipo kodi ndipo malamulo ake amatinji?

It's always them private nobody's 1😂😂😂🤣

@ThatGoodGuy01 Mafunso opoila pang’ono 😏😂

Feeling Entitled basi

Uniform yaku Admarc nde iti?

Ndiye pali chifukwa cimpatsira 5 years ngati waba ndalama?

😅😅💔 yaku admarc mulibe

Osavala uniform yaku ESCOM bwa

Uniform yaku Escom imawoneka bwa? Ma overall aja si uniform ya Escom bwana, akufunsa umbuli wa mzawo pomwe iwo nde mbuli yaku limbuli.

Koma nde kukokomezatu

Voice ya Salim chazama iyiyotu 🤣🤣🤣

Kungomulanda off you go bas, no need for all that drama. Komanso what's so special in wearing military Stuff? Aaaah

Mpaka uniform yaku maternity

this is not cool

Akufusa zau savage bwanao😂

Salimu Chazama ntchito zake zolowera pa window'zo!

Ati yaku matenite
